Wokhudza ife
Masomphenya
TWR imachotsa kusamvana pachiyankhulo ndipo onse oifikla angthe kuona kapena kuwerenga mauthenga a Chikhristu ndikukula mumayendedwee awo ndi Khristu.
Utumiki
TWR360 imafikila anthu ogwwiritsa ntchito intaneti ndi mafoni ammanja popitiliza utumiki othandizila Mpingo kukwaniritsa Lamulo la Khristu lolakila pa dziko lonse lapansi
- Kuthandiza wina aliyense pena pali ponse kuti kupyolera pa komputer kapena ma foni kupeza zowerenga zauzimu muchinenero chake
- Kupeleka kwa ofalitsa uthenga achi Khirisitu ndi njira zosiya siyana zopelekera uthenga, kwa iwo pamodzi ndi mautumiki akulu ndi ang'ono mwe.
- Kugwira ntchito ngati malo a ntchito a pakati kati kumene mapologalamu ochuluka a TWR360 amapezeka kupyolera mwa mapologalamu owulutsidwa popanda kutaya nthawi ndi choletsa china
wokhudza TWR
Speaking fluently in 200+ languages and dialects, TWR exists to reach the world for Jesus Christ. Our global media outreach engages millions in more than 160 countries with biblical truth. For more than 70 years, God has enabled TWR to help lead people from doubt to decision to discipleship.
Pamodzi ndi anzathu akunja, a mipingo, ndi mautumiki ena, TWR imakupatsilani zoulutsa zofunikira kuphunzitsa kukhala ophunzira wa Yesu ndi ogwira ntchito odzipeleka popereka chiyembekezo kwa anthu, ndi mamidzi ozungulira dziko lonse lapansi. Khaya pogwiritsa ntchito zida zamphamvu za AM/MW za wailesi, shortwave kapena FM komanso pa intaneti mwinanso pokumana nao omvera pamaso, TWR imasiya chilimbikitso chokhalitsa cha uzimu