N'chifukwa Chiyani Olungama Amwalira?
Wokondedwa mnzanga, ngati unadzifunsapo funso lokuti: “Chifukwa chiyani olungama amamwalira achichepere?” ndili nawe uthenga wabwino: Mulungu sakudziwa chabe za imfa ya munthu ali yense olungama, koma amasamala za ovutika, ndipo amakhala opezekeratu kwa iwo amene ali m’mavuto.
Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?
Ife, maka maka kuukira kwathu kwa zabwino ndi Mulungu wachikondi ndilo vuto leni leni. Khalani nafe tsopano pamene tikumaliza masewero athu, mafunso ovuta okhuza Mulungu, ndipo tiunika funso lomaliza komanso losautsa: “Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?”
Chithunzithunzi cha Mulungu
Zikhalidwe zakale za ku Asia ndi Indonesia kufikira kufikira anthu amasiku ano opezeka ku America ndi Africa, kulambira Mulungu sikwachilendo. Koma, kodi Mulungu ndi ndani? Kodi timadziwa chiyani za Iye?
MULUNGU NDI ATATE ATHU AKUMWAMBA
Zimaoneka ngati kufunafuna Mulungu ndi mbali imodzi imene imaonetsera umunthu wathu. Koma kodi munayamba mwadzifunsapo mafunso akuti -“Kodi Mulungu ndi ndani”, kapena “Kodi Mulungu ndi otani kwenikweni?” Nanga zimene timadziwa kwenikweni za iye ndi zotani?
Kodo Mulungu Amasamala Za Ine?
Funso limene amafunso silokuti, “Kodi ndidya usiku uno?” koma “koma ndidzadyanso?”