Mu phunziro la mapangano lino, tikuona ntchito za Mulungu Mlengi pokhudzana ndi munthu cholengedwa chake. Gwero lokhalo la chidziwitso limapezeka m’mavumbulutso a Mulungu mwa Iye mwini m’Malemba Oyera.
Chipangano Chosungira (Chipangano cha Nowa)
Ikani ku zokonda