Chipangano cha Ulamuliro (Chipangano cha mu Edeni)

Mawu akuti chipangano omwe agwiritsidwa ntchito m’Baibulo akukhudza zochita za Mulungu kapena ubale wake ndi munthu. Nthawi zonse Mulungu ndiye amakhazikitsa mfundo za chipanganochi. Ichi ndi chinthu chofunika kwambiri pakumvetsa kwathu mapangano. M’mapangano kapena m’zigwirizano pakati pa anthu, pakhoza kukhala kukambirana komanso kunyengererana. Koma sizili choncho ndi mapangano amene Mulungu anapanga.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.