Mulungu wa Chivumbulutso

Ndikukhulupirira kuti aliyense ali ndi lingaliro linalake la Mulungu. Ndinafunsa mnzanga wina, Dr. Joseph Ajayi, wochokera ku Nigeria, momwe amamvera pankhaniyi. Sanabadwire m'banja lachikhristu. Ndinamufunsa. "Podziwa zipembedzo za m'dziko lanu, kodi munganene kuti aliyense ali ndi chikhulupiriro choyambira chakuti kwinakwake kuli Mulungu?"

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.