MMENE MUNGAKHALIRE BWINO

Aliyense ayenera kulakalaka kukhala ndi moyo wabwino. Tikudziwa kuti pali njira yoyenera ndipo pali njira yolakwika. Tikudziwa zimenezo mkati mwa mitima yathu. Komabe, si aliyense amene amadziwa kukhala ndi moyo wabwino. Tiyenera kuphunzitsidwa momwe tingakhalire ndi moyo wabwino chifukwa popanda thandizo palibe amene angakhale ndi moyo wabwino. Baibulo limatiuza kuti si kwa munthu kulamulira mapazi ake.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.