MAGANIZO AMAYANG’ANIRA MMENE MUNTHU AMAKHALIRA

Yesu anali kutchula mawu a munthu wanzeru kwambiri amene anakhalako padziko lonse pamene anati, “Monga munthu amaganizira mumtima mwake, momwemonso aliri.” Ndikufuna kuti musinkhesinkhe pa zimenezo. M’maganizo mwathu timatsimikizira mmene timakhalira. Ngati muganizira zoyipa mudzachita zoyipa. Ngati muganizira zabwino mudzachita zabwino. Koma sitingathe nthawi zonse kugwiritsa ntchito zimenezo m’njira imeneyo. Ndili womasuka kuvomereza kuti nthawi zina maganizo anga sabweretsa zochita monga momwe ndikanayembekezera.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.