Chifukwa sitingathe kuona Mulungu, nthawi zambiri timafunsa umboni wakuti alipo. Nthawi zina timafuna tithe kuona Mulungu. Amuna a Mulungu a nthawi zapitazo analinso ndi chilakolako chofanana chimenechi. Komabe, anthu ena sangathe kuona chimene chili poyera.
KODI MULUNGU ALIPODI?
Ikani ku zokonda