Ndi chowonadi cholemekezeka chimenecho, bwenzi, chomwe inunso mungachite. Chochitika chimenecho cha kukhala mwa Khristu chimasintha maunansi m’moyo. Maunansi akale anatilumikiza ku dziko lapansi, thupi ndi ana a mdima. Paulo analemba za maunansi atsopanowo m’zochitika za moyo.
Maubale Athu Atsopano
Ikani ku zokonda