Pakuona ndi kuphunzira kwanga, ndaphunzira kuti pali zipembedzo mazana ambiri padziko lapansi. Chilichonse chili ndi ziphunzitso zake zapadera. Anthu ena amasokonezeka ndipo amadabwa kuti ndi chipembedzo chiti chomwe chili cholondola.
NJIRA YOKHAYO YOLONDOLA
Ikani ku zokonda