Tanthauzo la Pangano

Mulungu ndiye Wochita Wamkulu m'chilengedwe chonse makamaka padziko lapansi lino. Amalamulira zonse (Yesaya 40:10-31). Komabe mu ulamuliro Wake anasankha kulenga munthu, monga chifaniziro Chake amene wakhazikitsa naye ubale wapadera komanso wapamtima. Ubale umenewu si mgwirizano, kutanthauza kuti, awiri pamlingo womwewo. M'malo mwake ndi ubale wa Ambuye wachikondi wachifundo ndi mtumiki Wake wodzichepetsa womvera.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.