Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?

Ife, maka maka kuukira kwathu kwa zabwino ndi Mulungu wachikondi ndilo vuto leni leni. Khalani nafe tsopano pamene tikumaliza masewero athu, mafunso ovuta okhuza Mulungu, ndipo tiunika funso lomaliza komanso losautsa: “Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?”