Mafunso Okhudza Mulungu

Kodi kunja kuno kuli Mulungu? Chabwino. Nanga milungu ilipo yochuluka motani? Kodi ungadziwe bwanji kuti Mulungu alipo? Mungathe kumuona?

Mafunso Oonjezera Okhudza Mulungu

Kodi Mulungu amayang’ana aliyense pansi pano kufunitsitsa kutigwira tikalakwitsa? Kodi Mulungu amadziwa zomwe ndimachita mu mdima? Kodi munthu angamubisalire Mulungu? Mulungu ali kuti? Ngati sitingathe kumuona, tidziwa bwanji komwe ali?

Mafunso Okhudza Yesu

Yesu ndi ndani? KODI YESU NDI MULUNGU? Ndimaona ngati Yesu ndi munthu. Ndiye angakhale bwanji Mulungu? Chenicheni ndi chiti, Mulungu, kapena munthu?

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera