Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?

Ife, maka maka kuukira kwathu kwa zabwino ndi Mulungu wachikondi ndilo vuto leni leni. Khalani nafe tsopano pamene tikumaliza masewero athu, mafunso ovuta okhuza Mulungu, ndipo tiunika funso lomaliza komanso losautsa: “Chifukwa chiyani choipa chimaoneka ngati chimapambana?”

Chithunzithunzi cha Mulungu

Zikhalidwe zakale za ku Asia ndi Indonesia kufikira kufikira anthu amasiku ano opezeka ku America ndi Africa, kulambira Mulungu sikwachilendo. Koma, kodi Mulungu ndi ndani? Kodi timadziwa chiyani za Iye?

MULUNGU NDI ATATE ATHU AKUMWAMBA

Zimaoneka ngati kufunafuna Mulungu ndi mbali imodzi imene imaonetsera umunthu wathu. Koma kodi munayamba mwadzifunsapo mafunso akuti -“Kodi Mulungu ndi ndani”, kapena “Kodi Mulungu ndi otani kwenikweni?” Nanga zimene timadziwa kwenikweni za iye ndi zotani?

Yesu ndi Mulungu

Popeza ndi anthu ochepa amene ananenapo kuti amalankhulana ndi Mulungu, komanso ocheperabe anena kuti amamuona Mulungu maso ndi maso; ndiye tingadziwe bwanji kuti Iye ndi otani?

Kodi Kuli Mulungu?

Ngati munadwalapo nthenda yoopsya, kapena kuzunzidwa ndi munthu wina, mwina kugonapo ndi njala, kukhala opanda pogona, zovala, zikhoza kutheka kuti munafunsapo funso ngati ena ambiri: m’dziko la zowawa zochuluka, mukhoza kukhaladi Mulungu amene akuyang’anaira zonse?

Kodo Mulungu Amasamala Za Ine?

Funso limene amafunso silokuti, “Kodi ndidya usiku uno?” koma “koma ndidzadyanso?”

Kodi ndidzadyanso ine?

Ngati muli ngati ambiri mwa ife, ndiye kuti mwina munaona kale kuti dzikoli ndilodzaza ndi abambo ndi amayi amene akukhala mu nyengo ya zovuta, kuvutika tsiku ndi tsiku kungofuna kuti akhale moyo ndi kupeze chakudya komanso kokhala ndi banja lawo. Funso lomwe amadzifunsa silokuti “kodi ndidya chani madzulo ano?”, koma lokuti “Kodi ndidzadyanso ine?”

N'CHIFUKWA CHIYANI MULUNGU AMATULUTSA KUCHITSA KWAMBIRI? 1

Funso lomveka bwino limene iwo amafunsa ndi lokuti: Ngati Mulungu alipodi, ndipo ngati amatikondadi, n’chifukwa chani amalowa masautso ochuluka chomwechi? Okondwedwa, ngati munakumanapo . . .

N'CHIFUKWA CHIYANI MULUNGU AMATULUTSA KUCHITSA KWAMBIRI? 2

ndi chifukwa chiyani anthu ena amadutsa m’nyengo zokhoma, zowawa, pamene ena amadutsa m’nyengo zofewa zokha zokha?M’dziko limene dzuwa limawala komanso mvula imagwa mofanana kwa wina aliyense popanda tsankho, kodi chilungamo chili pati?

N'chifukwa Chiyani Olungama Amwalira?

Wokondedwa mnzanga, ngati unadzifunsapo funso lokuti: “Chifukwa chiyani olungama amamwalira achichepere?” ndili nawe uthenga wabwino: Mulungu sakudziwa chabe za imfa ya munthu ali yense olungama, koma amasamala za ovutika, ndipo amakhala opezekeratu kwa iwo amene ali m’mavuto.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera