Maubale Athu Atsopano

Ndi chowonadi cholemekezeka chimenecho, bwenzi, chomwe inunso mungachite. Chochitika chimenecho cha kukhala mwa Khristu chimasintha maunansi m’moyo. Maunansi akale anatilumikiza ku dziko lapansi, thupi ndi ana a mdima. Paulo analemba za maunansi atsopanowo m’zochitika za moyo.

NJIRA YOKHAYO YOLONDOLA

Pakuona ndi kuphunzira kwanga, ndaphunzira kuti pali zipembedzo mazana ambiri padziko lapansi. Chilichonse chili ndi ziphunzitso zake zapadera. Anthu ena amasokonezeka ndipo amadabwa kuti ndi chipembedzo chiti chomwe chili cholondola.

Kukhalanso ndi Moyo Mwa Yesu

Moyo Wochuluka

Matamando a Ulemelero Wake

Chifuniro Chabwino Cha Mulungu

Kufunikira Kopanga Chisankho

Kukhala Moyo Wotsimikizika

Chiyembekezo Changa – 546

Chiyembekezo Changa – 545

Chiyembekezo Changa – 544

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.