MMENE MUNGAKHALIRE MKHRISTU WOONA

alibe amene amakonda anthu achiphamaso. Anthu amene amaoneka ngati sali zomwe ali. Anthu amene amadzibisa nkhope ndikuonetsa umunthu wabwino kwambiri kuposa momwe alili. Ife timakonda anthu oona mtima ndi okhulupirika, amene ali mkati momwe aliri kunja.

KODI MULUNGU ALIPODI?

Chifukwa sitingathe kuona Mulungu, nthawi zambiri timafunsa umboni wakuti alipo. Nthawi zina timafuna tithe kuona Mulungu. Amuna a Mulungu a nthawi zapitazo analinso ndi chilakolako chofanana chimenechi. Komabe, anthu ena sangathe kuona chimene chili poyera.

CHINSINSI CHACHIKULU CHA MULUNGU CHAVUMBULUTSIDWA

Zoonadi, maganizo a Mulungu angakhale ndi zinsinsi zazikulu. Lingaliro lenilenilo lakuti Mulungu amadziwa zonse ndi lalikulu kuposa momwe maganizo athu angathe kuzindikira. Sanatiuze zonse zimene Iye amadziwa. Ayi, ayi konse.

NDONDOMEKO YODABWITSA YA Uthenga Wabwino

Tonse timagwirizana kuti palibe amene ayenera kuyesa kugwira ntchito osadziwa zomwe akuchita. Ntchito zambiri zimafuna ndondomeko kuti zichitike.

Maubale Athu Atsopano

Ndi chowonadi cholemekezeka chimenecho, bwenzi, chomwe inunso mungachite. Chochitika chimenecho cha kukhala mwa Khristu chimasintha maunansi m’moyo. Maunansi akale anatilumikiza ku dziko lapansi, thupi ndi ana a mdima. Paulo analemba za maunansi atsopanowo m’zochitika za moyo.

NJIRA YOKHAYO YOLONDOLA

Pakuona ndi kuphunzira kwanga, ndaphunzira kuti pali zipembedzo mazana ambiri padziko lapansi. Chilichonse chili ndi ziphunzitso zake zapadera. Anthu ena amasokonezeka ndipo amadabwa kuti ndi chipembedzo chiti chomwe chili cholondola.

Kukhalanso ndi Moyo Mwa Yesu

Moyo Wochuluka

Matamando a Ulemelero Wake

Chifuniro Chabwino Cha Mulungu

Kufunikira Kopanga Chisankho

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.