Tiona Ntchito Zokaikitsa Za Mkristu
-
Aroma 14:1-5
Close
Mmene Mkristu Ayenera Kukhalira Ndi Boma
Mkristu abvale Yesu mwa mau a Mulungu.
Kuchitira Umboni Kumpingo Ndi Kudziko Lonse
Uchimo wonse ukuchitika pamene Mulungu akuona ndipo ali ndi mphamvu yotsitsa boma lililonse limene likuchita kusamvera.
Kagwiridwe Ka Ntchito Mumpingo
Wokhulupirira ayenera kukondana ndi chikondi chachibadwidwe.
Paulo Akuumba Mkota Chiphunzitso Chake
Chifuniro cha munthu chimaoneka chabwino pamene moyo wa munthu wakonzekanso
Israyeli Abwezeretsedwa Mchikonzero Cha Mulungu
Israyeli adzatsekedwabe m'maso ndi kuumitsa mitima yawo kufikira nthawi ya mkwatulo.
A Yuda Wotsalira Kuchionongeko Pamodzi Ndi Amitundu, Adzapulumuka
Mulungu amapereka kuwala ndi cholinga chakuti munthu aone. Koma munthu akakhala wakhungu, sangaone.
Chipulumutso Chimaperekedwa Mwachisomo Kwa A Yuda Ndi Anthu Amitundu
Kubvomereza Kristu pakamwa, kuyenera kugwirizana ndi mtima.
Kusankhidwa Kwa Israyeli Ndi Mulungu
Ngakhale Mulungu amadana ndi tchimo koma amaleza mtima kupereka mwayi kwa anthu onse kuti adze kwa Iye mwakulapa machimo awo.
Tanthauzo La Dzina La Israyeli Kapena Kuti Chomwe Dzina La Israyeli Liimira
Kristu anadza ku mtundu wa Israyeli ngati mwana amene ndi mu Yuda weniweni. Koma akuimira Israyeli ndi mitundu yonse ya dziko lapansi.
Kutetezedwa Kwa Wokhulupirira
Pamene tikamba nkhani ya chipulumutso ndiye kuti tikukamba za chipulumutso.