Kusanthula Baibulo
-
Akolose 3:1
Close
Kusanthula mau pawekha nkopindulitsa
Kuwerenga Baibulo
Powerenga Mau yambani ndi pemphero
Pemphero ndi lofunika kuti timve zomwe Mulungu akulankhula kwa ife mu Mau ake
Kufunika kwa mau otsogolera
Kutanthauzira mau ena okhuzana ndi Baibulo
Baibulo lichokera kwa Mulungu
Mulungu ndi amene analankhula ndi anthu ake mmalemba
Kufunika kwa Baibulo
Baibulo ndi lofunika pamoyo wa aliyense